Gawo 1: Masomphenya a Umodzi wa Mpingo

Written by Paul J Bucknell on January, 24, 2024

Gawo 1: Masomphenya a Umodzi wa Mpingo

Masomphenya ndi Ndondomeko za mpingo zimayenera kukhazikika pa Mau a Mulungu.  Pamene talandira nzeru ndi kutsatira Malangizo ake, maganizidwe athu osinthika akhoza Kugwira ntchito molunjika kukukwaniritsidwa kwa umodzi wa mpingo mosasemphana ndi Malangizo opezeka m’Mau a Mulungu.  Ndichinthu chofunikira kwambiri kuwona chinthu cha mtengo wapatali umodzi wa mkazi wa Khristu ndi kugwirira ntchito pamodzi pa zinthu zimene zimatimangirira pamodzi – Yesu Khristu – kusiyana ndi zimene zimatigawanitsa.

Comments

There are currently no comments, be the first!


We noticed you're not logged in, please login before commenting, thank you!

Related Articles

-->